Numeri 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Padzafika zombo zochokera kugombe la Kitimu,+Ndipo iwo adzasautsa Asuri+ ndithu,Adzasautsadi Ebere.Koma iyenso adzawonongeka pamapeto pake.” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:24 Nsanja ya Olonda,10/15/2007, ptsa. 18-19
24 Padzafika zombo zochokera kugombe la Kitimu,+Ndipo iwo adzasautsa Asuri+ ndithu,Adzasautsadi Ebere.Koma iyenso adzawonongeka pamapeto pake.”