Numeri 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amenewa anali mabanja a Arubeni. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 43,730.+