Numeri 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna a Isakara+ ndi mabanja awo anali awa: Tola+ amene anali kholo la banja la Atola, Puva amene anali kholo la banja la Apuna,
23 Ana aamuna a Isakara+ ndi mabanja awo anali awa: Tola+ amene anali kholo la banja la Atola, Puva amene anali kholo la banja la Apuna,