Numeri 26:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Awa ndiwo anthu amene Mose ndi wansembe Eleazara anawawerenga pakati pa ana a Isiraeli. Anawawerengera m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko.+
63 Awa ndiwo anthu amene Mose ndi wansembe Eleazara anawawerenga pakati pa ana a Isiraeli. Anawawerengera m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko.+