Numeri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Bambo athu anafera m’chipululu.+ Koma iwo sanali nawo m’gulu la Kora+ limene linasonkhana kuti litsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo,+ ndipo pa nthawiyo analibe mwana aliyense wamwamuna.
3 “Bambo athu anafera m’chipululu.+ Koma iwo sanali nawo m’gulu la Kora+ limene linasonkhana kuti litsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo,+ ndipo pa nthawiyo analibe mwana aliyense wamwamuna.