Numeri 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku loyamba la chikondwererocho muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+
18 Pa tsiku loyamba la chikondwererocho muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+