Numeri 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwamunayo akam’kaniza pa tsiku limene wamva kulonjezako,+ ndiye kuti wafafaniza lonjezo la mkaziyo, kapena lonjezo lake limene anachita mosaganizira bwino, limene analumbirira moyo wake ndi pakamwa pake. Yehova adzam’khululukira mkaziyo.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:8 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 27
8 Mwamunayo akam’kaniza pa tsiku limene wamva kulonjezako,+ ndiye kuti wafafaniza lonjezo la mkaziyo, kapena lonjezo lake limene anachita mosaganizira bwino, limene analumbirira moyo wake ndi pakamwa pake. Yehova adzam’khululukira mkaziyo.+