-
Numeri 32:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 N’chifukwa chiyani mukufuna kuwatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asawolokere kudziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa?
-