Numeri 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Amuna amene anatuluka mu Iguputo kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ sadzaiona nthaka imene ndinalumbirira Abulahamu, Isaki ndi Yakobo,+ chifukwa sanandimvere ndi mtima wonse.
11 ‘Amuna amene anatuluka mu Iguputo kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ sadzaiona nthaka imene ndinalumbirira Abulahamu, Isaki ndi Yakobo,+ chifukwa sanandimvere ndi mtima wonse.