Numeri 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukaleka kumumvera,+ ndithu iye adzachititsanso anthu onsewa kukhalabe m’chipululu muno,+ ndipo mudzawazunzitsa kwambiri.”+
15 Mukaleka kumumvera,+ ndithu iye adzachititsanso anthu onsewa kukhalabe m’chipululu muno,+ ndipo mudzawazunzitsa kwambiri.”+