Numeri 33:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu n’kukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+
48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu n’kukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+