Deuteronomo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Nyamukani, muyende ndi kudutsa chigwa cha Arinoni.+ Taonani, ndapereka m’manja mwanu Sihoni,+ Mwamori, mfumu ya Hesiboni. Yambani kulanda dziko lake, ndipo menyanani naye nkhondo.
24 “‘Nyamukani, muyende ndi kudutsa chigwa cha Arinoni.+ Taonani, ndapereka m’manja mwanu Sihoni,+ Mwamori, mfumu ya Hesiboni. Yambani kulanda dziko lake, ndipo menyanani naye nkhondo.