Deuteronomo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ndinatembenuka, n’kutsika m’phirimo,+ ndipo ndinaika miyala iwiriyo m’likasa limene ndinapanga kuti izikhala mmenemo, monga mmene Yehova anandilamulira.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 31
5 Ndiyeno ndinatembenuka, n’kutsika m’phirimo,+ ndipo ndinaika miyala iwiriyo m’likasa limene ndinapanga kuti izikhala mmenemo, monga mmene Yehova anandilamulira.+