Deuteronomo 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo ine ndinakhala m’phirimo masiku ofanana ndi oyamba aja, masiku 40, usana ndi usiku,+ ndipo Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+ Yehova sanafune kukuwonongani.+
10 Ndipo ine ndinakhala m’phirimo masiku ofanana ndi oyamba aja, masiku 40, usana ndi usiku,+ ndipo Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+ Yehova sanafune kukuwonongani.+