Deuteronomo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Yehova anandiuza kuti, ‘Nyamuka, tsogolera anthu kuti ayambe ulendo, kuti akalowe ndi kutenga dziko limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.’+
11 Kenako Yehova anandiuza kuti, ‘Nyamuka, tsogolera anthu kuti ayambe ulendo, kuti akalowe ndi kutenga dziko limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.’+