Deuteronomo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 mbawala yamphongo, insa, ngondo,+ mbuzi yakuthengo, mphalapala, nkhosa yakuthengo ndi chinkhoma.