Deuteronomo 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musadyenso nthiwatiwa,+ kadzidzi, kakowa ndi mtundu uliwonse wa kabawi.