Deuteronomo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mlendo+ ungam’kakamize kubweza ngongole, koma ngati m’bale wako wakongola chinthu chako chilichonse usam’kakamize kuchibweza.
3 Mlendo+ ungam’kakamize kubweza ngongole, koma ngati m’bale wako wakongola chinthu chako chilichonse usam’kakamize kuchibweza.