Deuteronomo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Uzim’kongoza m’bale wako mowolowa manja,+ mulimonse mmene iye wafunira atakupatsa chikole, ndipo uzim’kongoza zimene akusowa. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:8 Nsanja ya Olonda,9/15/2010, tsa. 8
8 Uzim’kongoza m’bale wako mowolowa manja,+ mulimonse mmene iye wafunira atakupatsa chikole, ndipo uzim’kongoza zimene akusowa.