Deuteronomo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola.+ N’chifukwa chake lero ndikukulamula zinthu zimenezi. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:15 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, tsa. 19
15 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola.+ N’chifukwa chake lero ndikukulamula zinthu zimenezi.