Deuteronomo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Mukazungulira mzinda kwa masiku ambiri mwa kumenyana nawo kuti muulande, musawononge mitengo yake mwa kuisamulira nkhwangwa. Muyenera kudya zipatso za mitengoyo, chotero simuyenera kuidula.+ Kodi mtengo wa m’munda ndi munthu kuti muwuukire? Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:19 Yandikirani, tsa. 135
19 “Mukazungulira mzinda kwa masiku ambiri mwa kumenyana nawo kuti muulande, musawononge mitengo yake mwa kuisamulira nkhwangwa. Muyenera kudya zipatso za mitengoyo, chotero simuyenera kuidula.+ Kodi mtengo wa m’munda ndi munthu kuti muwuukire?