Deuteronomo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muyezo wako woyezera kulemera kwa chinthu uzikhala wolondola ndi woyenera. Muyezo wako wa efa uzikhala wolondola ndi woyenera kuti masiku ako achuluke m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2022, tsa. 27
15 Muyezo wako woyezera kulemera kwa chinthu uzikhala wolondola ndi woyenera. Muyezo wako wa efa uzikhala wolondola ndi woyenera kuti masiku ako achuluke m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+