Deuteronomo 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anatibweretsa kumalo ano ndi kutipatsa dziko ili, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+