Yoswa 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma amuna achiisiraeli anayankha Ahiviwo+ kuti: “Mwinamwake mumakhala pafupi chakonkuno. Ndiye tingachite nanu bwanji pangano?”+
7 Koma amuna achiisiraeli anayankha Ahiviwo+ kuti: “Mwinamwake mumakhala pafupi chakonkuno. Ndiye tingachite nanu bwanji pangano?”+