Yoswa 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo poyankha anauza Yoswa kuti: “Ndife okonzeka kukhala akapolo anu.”+ Ndiyeno Yoswa anawafunsanso kuti: “Koma ndinu ndani makamaka, ndipo mwachokera kuti?”
8 Iwo poyankha anauza Yoswa kuti: “Ndife okonzeka kukhala akapolo anu.”+ Ndiyeno Yoswa anawafunsanso kuti: “Koma ndinu ndani makamaka, ndipo mwachokera kuti?”