Yoswa 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakumva zimenezi, akulu akwathu ndi anthu onse a m’dziko lathu anatiuza kuti,+ ‘Tengani kamba wa pa ulendo, mupite mukakumane nawo. Mukawauze kuti: “Ife ndife akapolo anu.+ Chonde chitani nafe pangano.”’+
11 Pakumva zimenezi, akulu akwathu ndi anthu onse a m’dziko lathu anatiuza kuti,+ ‘Tengani kamba wa pa ulendo, mupite mukakumane nawo. Mukawauze kuti: “Ife ndife akapolo anu.+ Chonde chitani nafe pangano.”’+