Yoswa 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo atsogoleri onse anauza khamu lonselo kuti: “Ife tinawalumbirira pali Yehova Mulungu wa Isiraeli, ndipo tsopano sitingawachitire choipa.+
19 Pamenepo atsogoleri onse anauza khamu lonselo kuti: “Ife tinawalumbirira pali Yehova Mulungu wa Isiraeli, ndipo tsopano sitingawachitire choipa.+