Yoswa 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse omwe anali naye anachoka ku Libina n’kupita ku Lakisi.+ Kumeneko anamanga msasa pafupi ndi mzindawo n’kuuthira nkhondo.
31 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse omwe anali naye anachoka ku Libina n’kupita ku Lakisi.+ Kumeneko anamanga msasa pafupi ndi mzindawo n’kuuthira nkhondo.