Yoswa 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa cha ana a Simiyoni chinali m’gawo la ana a Yuda chifukwa ana a Yuda gawo lawo linawakulira.+ Choncho ana a Simiyoni anapatsidwa malo pakati pa cholowa chawo.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:9 Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,11/2021, tsa. 2
9 Cholowa cha ana a Simiyoni chinali m’gawo la ana a Yuda chifukwa ana a Yuda gawo lawo linawakulira.+ Choncho ana a Simiyoni anapatsidwa malo pakati pa cholowa chawo.+