Yoswa 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ichi chinali cholowa cha fuko la ana a Isakara potsata mabanja awo,+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.
23 Ichi chinali cholowa cha fuko la ana a Isakara potsata mabanja awo,+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.