Yoswa 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yoswa anauza anthu onse kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kalekale, makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori,+ ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:2 Tsanzirani, tsa. 25 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, tsa. 118/15/2001, ptsa. 14-15
2 Tsopano Yoswa anauza anthu onse kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kalekale, makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori,+ ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.