Yoswa 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene ndinali kutulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pang’ono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira+ ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.
6 Pamene ndinali kutulutsa makolo anu ku Iguputo,+ atatsala pang’ono kufika kunyanja, Aiguputo anawathamangira+ ndi magaleta ankhondo ndiponso amuna okwera pamahatchi, mpaka ku Nyanja Yofiira.