Yoswa 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo, iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ine ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo,+ ndipo ine ndinawamiza ndi madzi a m’nyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako, inu munakhala m’chipululu masiku ambiri.+
7 Pamenepo, iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ine ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo,+ ndipo ine ndinawamiza ndi madzi a m’nyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako, inu munakhala m’chipululu masiku ambiri.+