Yoswa 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+
9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+