Yoswa 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine sindinafune kumvera Balamu.+ Chotero, iye anakudalitsani mobwerezabwereza,+ ndipo ine ndinakulanditsani m’manja mwake.+
10 Ine sindinafune kumvera Balamu.+ Chotero, iye anakudalitsani mobwerezabwereza,+ ndipo ine ndinakulanditsani m’manja mwake.+