Yoswa 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinawachititsa mantha inu musanafike, choncho anakuthawani+ monga anachitira mafumu awiri a Aamori. Iwo sanathawe chifukwa cha lupanga lanu kapena chifukwa cha uta wanu.+
12 Ndinawachititsa mantha inu musanafike, choncho anakuthawani+ monga anachitira mafumu awiri a Aamori. Iwo sanathawe chifukwa cha lupanga lanu kapena chifukwa cha uta wanu.+