Yoswa 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero ndinakupatsani dziko limene simunakhetsere thukuta ndi mizinda imene simunamange,+ ndipo inu munayamba kukhalamo. Ndiponso mukudya zipatso za mitengo ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene simunabzale.’+
13 Chotero ndinakupatsani dziko limene simunakhetsere thukuta ndi mizinda imene simunamange,+ ndipo inu munayamba kukhalamo. Ndiponso mukudya zipatso za mitengo ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene simunabzale.’+