Yoswa 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsopano opani Yehova+ ndi kum’tumikira mosalakwitsa ndiponso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje ndi ku Iguputo,+ ndipo tumikirani Yehova.
14 “Tsopano opani Yehova+ ndi kum’tumikira mosalakwitsa ndiponso mokhulupirika.*+ Chotsani milungu imene makolo anu ankatumikira kutsidya lina la Mtsinje ndi ku Iguputo,+ ndipo tumikirani Yehova.