Yoswa 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo Yoswa anauza anthuwo kuti: “Inu ndinu mboni mwa kufuna kwanu,+ zotsimikizira kuti mwasankha nokha kutumikira Yehova.”+ Ndiyeno anthuwo anati: “Inde! Ndife mboni.”
22 Pamenepo Yoswa anauza anthuwo kuti: “Inu ndinu mboni mwa kufuna kwanu,+ zotsimikizira kuti mwasankha nokha kutumikira Yehova.”+ Ndiyeno anthuwo anati: “Inde! Ndife mboni.”