Yoswa 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa tsikulo, Yoswa anachita pangano ndi anthuwo ndi kuwaikira lamulo ndi chigamulo+ ku Sekemu.