Yoswa 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yoswa anauza anthu onsewo kuti: “Taonani! Mwala uwu ukhala mboni yotsutsana nafe,+ chifukwa mwalawu wamva mawu onse amene Yehova walankhula kwa ife, ndipo ukhala mboni kwa inu kuti musadzakane Mulungu wanu.”
27 Kenako Yoswa anauza anthu onsewo kuti: “Taonani! Mwala uwu ukhala mboni yotsutsana nafe,+ chifukwa mwalawu wamva mawu onse amene Yehova walankhula kwa ife, ndipo ukhala mboni kwa inu kuti musadzakane Mulungu wanu.”