Oweruza 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 25
8 Pamenepo amuna a ku Efuraimu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi? Bwanji sunatiitane pokamenya nkhondo ndi Amidiyani?”+ Ndipo iwo anayesetsa mwamphamvu kuti achite naye mkangano.+