Oweruza 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero, anauzanso amuna a ku Penueli kuti: “Ndikabwerako bwino, ndidzagwetsa nsanja yanuyi.”+