Oweruza 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Gidiyoni anawauza kuti: “Anali abale anga, ana a amayi anga. Pali Yehova Mulungu wamoyo, sindikanakuphani mukanawasiya amoyo.”+
19 Pamenepo Gidiyoni anawauza kuti: “Anali abale anga, ana a amayi anga. Pali Yehova Mulungu wamoyo, sindikanakuphani mukanawasiya amoyo.”+