Oweruza 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anauza Yeteri mwana wake woyamba kuti: “Nyamuka uwaphe.” Koma mnyamatayo sanasolole lupanga lake chifukwa anachita mantha, pakuti anali akali wamng’ono.+
20 Ndiyeno anauza Yeteri mwana wake woyamba kuti: “Nyamuka uwaphe.” Koma mnyamatayo sanasolole lupanga lake chifukwa anachita mantha, pakuti anali akali wamng’ono.+