Oweruza 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo anawauzanso kuti: “Ndikupempheni chinthu chimodzi: Aliyense wa inu andipatse ndolo* yapamphuno+ kuchokera pa zimene wafunkha.” (Ogonjetsedwawo anali ndi ndolo zapamphuno zagolide, chifukwa anali Aisimaeli.)+
24 Ndipo anawauzanso kuti: “Ndikupempheni chinthu chimodzi: Aliyense wa inu andipatse ndolo* yapamphuno+ kuchokera pa zimene wafunkha.” (Ogonjetsedwawo anali ndi ndolo zapamphuno zagolide, chifukwa anali Aisimaeli.)+