Oweruza 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Delila+ anauza Samisoni kuti: “Iwe wandipusitsa pondiuza bodza.+ Tsopano ndiuze, chonde, zimene angakumange nazo.”
10 Kenako Delila+ anauza Samisoni kuti: “Iwe wandipusitsa pondiuza bodza.+ Tsopano ndiuze, chonde, zimene angakumange nazo.”