Oweruza 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Delila anauza Samisoni kuti: “Wakhala ukundipusitsa mpaka pano mwa kundiuza bodza.+ Ndiuze zimene angakumange nazo.”+ Poyankha Samisoni anati: “Uluke zingongo 7 za m’mutu mwanga ndi ulusi wa m’litali+ mwa nsalu.”
13 Kenako Delila anauza Samisoni kuti: “Wakhala ukundipusitsa mpaka pano mwa kundiuza bodza.+ Ndiuze zimene angakumange nazo.”+ Poyankha Samisoni anati: “Uluke zingongo 7 za m’mutu mwanga ndi ulusi wa m’litali+ mwa nsalu.”