-
Oweruza 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Delila ataona kuti Samisoni wamuululira zonse za pansi pa mtima wake, nthawi yomweyo anatumiza mthenga kukaitana olamulira ogwirizana a Afilisiti,+ kuti: “Bwerani tsopano popeza wandiululira zonse za pansi pa mtima wake.”+ Pamenepo olamulira ogwirizana a Afilisiti aja anabwera kwa Delila ndipo anam’patsa ndalama.+
-