1 Samueli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene anali kupemphera choncho kwa Yehova kwa nthawi yaitali,+ Eli anali kuyang’anitsitsa pakamwa pake.
12 Pamene anali kupemphera choncho kwa Yehova kwa nthawi yaitali,+ Eli anali kuyang’anitsitsa pakamwa pake.